Stream and Download M-One - Ghetto Master Feat. Macelba (Prod. Janta)
MalawiHostit is a Malawian Top Web hosting Company.
(Intro!!!!)
Yeah!! "yeah!!!!", put ur, put ur, put ur hands up
Yeah!!! Ah!! Put ur!
Hook//
That time when l was in the Ghetto
Fanz yose yikanditcha ine master
Ndikatchilitsa mabebi drunken master
Pano ndinapanga mbiri ngati ndine Rasta!!!! Yeah!!!! ×2
Verse 1 // M-One
Ghetto Zingwangwa, Chilobwe, Ndilande,
23, 25, Chiwavi!!!
Ndinapanga mbiri/,
komasi ambiri omwe angapange mbiri
Fusafusa kwa Neba akuwuza mbiri /
Akuwuza okha kuti ndine katwiri/
Phechepepe mwanjovu sitimalowamo kawiri
Ngakhale flow yayine sindimabwerezaso kawiri
*Usaphweketse Ghetto coz fana okulira mu Ghetto.
Amaziwa ngini,
Ma Sley queen amu Ghetto Amaziwa life.
Vibe yamu Ghetto fana Hood singamake.
Ndati singamake fana Ghetto muli Gist.
Fanz yamu Ghetto fana iwe anakoza.
Kaya ndima demo fana iwe timamatcha.
Ndinapha chiwanda chamaluzi mu Ghetto pano ndili ndi dollar.
Ma tracks anga ose Ndinapha,
Apolice akundisa pano ati ndili ndi mulandu wa murder.
( Hook)
Verse //2 Macelba
Moyo wachiletso ndakulira pa phepo.
Fana waku Gutter ndakulira mu Ghetto.
Kuphura njerwa, njerwa zija zamoto.
Koma osagwa ulesi one day zawina rotto.
Pano ndimadziwa Magaye amandiva.
Fana wamu Ghetto anasanduka leader.
Kuyambira BT paka ku Khata-bay.
Olo ndikhale amandikambe .
Kawale, 2 far komaso ndix Ghetto .
Amayijaja Zimacelba ndizanyimbo.
Ndeee, sindifooka ndinachokera ku Ghetto ,
Ukandiphweketsa fana yizakushosha ndi Ghetto weee!!! .
(Hook)
Meet Eliza Mponya a Malawian Gospel Artist.