Stream and Download Tescal - Tsamba [Prod. LCB Studios]
										Intro 
From startiiieeeee 
 
LCB 🗣️🗣️ 
 
From start to the end you know / 
End you  know / 
 
 Hook 
I'm just di hustler Sindimaziwa saraly yeeeh/ 
Kuyesesa umu ndi umu kut kathupi kasalaleeee yeeeh/ 
Mpamba ndilibe / 
Or Tsamba ndilibe / 
Kuyesa yaugwanya ati akufuna Tsamba / 
Nanga yokolopa ati akufuna Tsamba / 
Tsamba Tsamba Tsamba chilichose ndi Tsamba / 
Chilichose ndi Tsamba Tsamba Tsamba chilichose ndi Tsamba / 
Tsamba Tsamba Tsambaaaaaaaaa/ 
 
 Ves 1 
Ndinagwirako jane 
Grace ka nurse / 
Ananditaya palipose ati ndilibe Tsamba / 
Sakufuna daily azikadya masamba/ 
Kuyesa yapa gate Ati afuna Tsamba / 
Moyo ukuwawa zizayenda liti mawa/ 
I feel like I'm drowning when I think about my future / 
Chomwe chimawawa ndikusamba njeee mafuta/ 
Magobo every time kut ndiwo ndithire mafuta/ 
 
 Back to hook  
 
 Ves 2  
 
As you already know kut dziko linavuta/ 
Ngati ulibe Tsamba sungapeze chochita/ 
What you need is just work hard / 
Osatopa Osafooka ma move kuma studer/ 
Osanama mnali shasha wapa secondary / 
Koma zonse man zinali za temporary / 
Kuiwala lero simawa/ 
Zibwana tinkapanga class kumathawa/ 
Lero siizi kuchita kusowa soap/ 
Magobo everytime kuti timweko Sobo/ 
Lero siizi kuchita kusowa soap/ 
Magobo everytime kuti timweko Sobo/ 
 
 Hook  
 
 Hook									
