Published 4 years ago in Other
malawitunesads malawitunesads malawitunesads malawitunesads
  • 277
  • 866
  • 1
  • 0
  • 3
  • 0

Download: Piksy - Sandra

Malawi Hostit

MalawiHostit is a Malawian Top Web hosting Company.

Lyrics

Song Lyrics: Sandra

(Verse 1)
Ntima wanga unakonda zina unakana,
Zina wakana dzina langa lomaliza lidzakukhala,
Lidzakukhala chili chonse pa iweyo chiri nchimake,
Oh sweet Sandra, oh sweet sandra I’m working hard kuti one day my dear udzakhale wanga, wanga Sandra.

[Chorus]
Oh my dear Sandra
Umandiwaza
One day nzasanja
Then you will be my sandra
Oh my dear Sandra
Umandiwaza
One day nzasanja
Then you will be my sandra

[Verse 2]
I know amanena miseche (miseche),
Kuti ndidzathela m’maloto,
I’m praying zinthu ziyende,
That i prove them wrong,
Mofatsa, mwa mwano
Ndimakufeela more
Mokwiya, moseka
Oh-oh.

[Chorus]
Oh my dear Sandra
Umandiwaza
One day nzasanja
Then you will be my sandra
Oh my dear Sandra
Umandiwaza
One day nzasanja
Then you will be my sandra

Sandra, sandra, umandiwaza
Sandra, sandra, timange banja

Oh my dear Sandra
Umandiwaza
One day nzasanja
Then you will be my sandra

::
/ ::

Queue

Clear