Mamawa omwe Uno kwachitika Ngozi yowopsya Ku mulanje 
					
						Francis Yolam - 
						منذ 5 سنوات
					
					Pomwe galimoto yaikuru kapena ena amati galimoto ya chimbayambaya track lnakawomba minibus. Kwa ena zithunzi za ngoziyi ndizowopsya kwambiri chifukwa  anthu ena aduka mikono komaso miyendo pamalo angoziwo.