Meet Bessing Leonard is Lilongwe based gospel artist. She started doing music in 2013 after being inspired by Clara Nguluwe . Blessing watulusapo nyimbo zingapo zomwe anthu ambili amazikonda. Ndipo 2022 sakupuma chifukwa iye akufuna uthenga wambuye ukafike madela omwe iye sangakwanise kufika ndiku sitha miyoyo ya anthu kudzela munyimbo zake.
admin
0 comments