Published 2 years ago in Poem's
malawitunesads malawitunesads malawitunesads malawitunesads
  • 1,217
  • 4,547
  • 2
  • 0
  • 5
  • 0

A gospel poem by Robert Chiwamba featuring the legendary Nepman. Inspired by 2 Timothy 4:8, the poem encourages born again christians to persevere in order not to lose the crown of life preserved for those that shall stand Christ till the end.

Malawi Hostit

MalawiHostit is a Malawian Top Web hosting Company.

Lyrics

Nepman (hook)
Ndikagwira ntchito, yambuye wangayo, ndidzalandira Kolona
Kolonayo,
Kolona Kolona Kolona Kolona, Ndidzalandira Kolona
Kolonayo
Kolona Kolona, Kolona, Kolona ndidzalandira Kolona
Chiwamba ( verse 1)
Pamapeto pa zonse tidzafika kumudzi wathu
Kukumana nayo mfumu ya mafumu yachilungamo
Ndachita bwino mtima ukugunda ndidzadzifunsa
Alikuti wanga Kolona yamafumu mfumu ndidzaifunsa
Unapilira Ku mayesero ima apa
Chizindikiro cha mtanda unali nacho khala apa
Unalolera kusauka kamba kamtanda sunthira apa
Angelo nonse ombani mmanja
Pamene Kolona akuvekedwa wanga mwana
Ndikulindilira langa tsikulo
Lomwe adzapukute yonse misonzi
Kukwera mtengo kwazinthu, ulova, njala
Nandiyitana
Okalandira wanga Kolona.
Nepman ( Bridge)
Kolona, Kolona, Kolona, Kolona, ndidzalandira, Kolona
Kolonayo
Chiwamba ( Verse 2)
Mlonda nthawi ili bwanji
Kunja tsopano Kuli kucha
Owerenga khala maso
Wanzeru apenye dzuwa
Zizindikiro nde zukwana
Zachuma kusokonelera padziko lonse
Madzi kusefukira nthawi zonse
Nkhondo zoopsa ponseponse
Mutanganidwiranjinso ndi dziko
Mutamandiranjinso maphunziro
Chuma sichingakupulumutseni Ku mkwiyo
Ndinthawi loliyatsa wa Kwa Yesu liwiro
Uku tikufuula ndisungireni Kolona yo
Ndikamaliza ntchitoyi ndzalandira
Chiwamba ( Verse 3 )
Olema ndi othodwa idzani
Ovutika mthupi odwala chirani
Anjala, osowa chiyembekezo fikani
Yesu manja watambalalitsa pamtanda
Mu nyengo zovutazi kufuna kukumbatirafe
Kuli mphoto Kwa yense oyima chiliri mpaka kumapeto
Sitikugwira ntchito yabule
Atisungire kolonayo
Tikamaliza ntchitoyi
Tidzalandira

Nice!! mumatha🙌🙌

::
/ ::

Queue

Clear