Published 3 months ago in Afro
malawitunesads malawitunesads malawitunesads malawitunesads
  • 276
  • 1,488
  • 0
  • 0
  • 12
  • 0
  • 0

Joseph Nkasa : TITHAWIRE KWA IYE

1.Pena ndumazifunsa chikuchitika ndi chani? Kapena ndikulota nthawi ina ndigalamuka.
Ayi simaloto zikuchitika reality, tili mmasiku otsiriza.

Lyrics

Joseph Nkasa : TITHAWIRE KWA IYE

1.Pena ndumazifunsa chikuchitika ndi chani? Kapena ndikulota nthawi ina ndigalamuka.
Ayi simaloto zikuchitika reality, tili mmasiku otsiriza.
Kumuona mneneri munthu wa Mulungu akutafuna gondolosi ,mankhwala achikuda.
Kubwira tseketseke kunyambita chiswa B , umangodziwiratu wonyenga uyu
Mu service yawo amakonda azimayi kuwapasa uneneri akuwagwiragwira, service ikatha amayi musalile , akunama akufuna mupange nawo chisembwere
Amayu ochuluka, mmilaga ndi malipondo akulera ana a anthu a Mulungu
Amapita kuti akapemphereredwe vuto lawo mirakuli inakachitikira ku room.
#Chorus
Manyasa! Tithawire kwaiye,
Manyasa! Tithawire kwaiye
Manyasa! Tithawire kwa mtsogoleri wopanda chinyengo

Iye amene anali! Tithawire kwaiye
Ndiamene ali! Tithawire kwaiye
Ndiamene ali nkuza! Tithawire kwa mtsogoleri wa Chilungamotu

Chimene amalonjeza! Tithawire kwaiye
Ndichimene amachita! Tithawire kwaiye.
Salonjeza osachita! Tithawire kwa msamariya wachifundo

Pamene moyo ukulimba! Tithawire kwaiye
Katundu kukwera daily! Tithawire kwaiye
Wosazimva! Tithawire kwa woyamba wotsiriza!!!

2 .To be continued. /

Nyimboyi sanaonese mbali wasakatulamo olamula ndi otsutsa omwe.

:
/ :

Queue

Clear