Mamawa omwe Uno kwachitika Ngozi yowopsya Ku mulanje
Francis Yolam -
5 years ago
Pomwe galimoto yaikuru kapena ena amati galimoto ya chimbayambaya track lnakawomba minibus. Kwa ena zithunzi za ngoziyi ndizowopsya kwambiri chifukwa anthu ena aduka mikono komaso miyendo pamalo angoziwo.